Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 22:28, 29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ngati mwamuna wakumana ndi namwali amene sanalonjezedwe ndi mwamuna kuti adzamukwatira ndipo wamugwira nʼkugona naye, ndiyeno agwidwa,+ 29 mwamunayo azipereka masekeli 50 asiliva kwa bambo a mtsikanayo, ndipo azikhala mkazi wake.+ Chifukwa chakuti wamuchititsa manyazi, sadzaloledwa kumusiya masiku onse a moyo wake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena