Genesis 50:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Potsirizira pake, Yosefe anauza abale ake kuti: “Ine ndikufa, koma Mulungu adzakuthandizani+ ndipo adzakutulutsani ndithu mʼdziko lino. Adzakupititsani kudziko limene analumbira kuti adzalipereka kwa Abulahamu, kwa Isaki ndi kwa Yakobo.”+ Ekisodo 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mose anatenganso mafupa a Yosefe chifukwa Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeli kuti: “Ndithudi, Mulungu adzakukumbukirani, ndipo pochoka kuno mudzatenge mafupa anga.”+
24 Potsirizira pake, Yosefe anauza abale ake kuti: “Ine ndikufa, koma Mulungu adzakuthandizani+ ndipo adzakutulutsani ndithu mʼdziko lino. Adzakupititsani kudziko limene analumbira kuti adzalipereka kwa Abulahamu, kwa Isaki ndi kwa Yakobo.”+
19 Mose anatenganso mafupa a Yosefe chifukwa Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeli kuti: “Ndithudi, Mulungu adzakukumbukirani, ndipo pochoka kuno mudzatenge mafupa anga.”+