Ekisodo 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho anthuwo anaimabe patali pomwepo, koma Mose anayandikira mtambo wakuda kumene kunali Mulungu woona.+ Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”
21 Choncho anthuwo anaimabe patali pomwepo, koma Mose anayandikira mtambo wakuda kumene kunali Mulungu woona.+
8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”