Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yamgwirizano*+ kwa Yehova ndipo akufuna kupereka ngʼombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema. Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano lamulo la nsembe yamgwirizano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova ndi ili:
3 “‘Ngati akupereka nsembe yamgwirizano*+ kwa Yehova ndipo akufuna kupereka ngʼombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.