-
Ekisodo 18:25, 26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Mose anasankha amuna oyenerera mu Isiraeli monse kuti akhale atsogoleri a anthu. Anasankha atsogoleri a magulu a anthu 1,000, atsogoleri a magulu a anthu 100, atsogoleri a magulu a anthu 50 ndi atsogoleri a magulu a anthu 10. 26 Choncho iwo ankaweruza anthuwo pakakhala mlandu. Mlandu wovuta ankapita nawo kwa Mose,+ koma mlandu uliwonse waungʼono ankauweruza.
-