Ekisodo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ine ndidzalola Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zodabwitsa zochuluka mʼdziko la Iguputo.+ Ekisodo 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Aiguputo anayamba kuumiriza anthuwo kuti achoke mʼdzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+ Deuteronomo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Yehova anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zazikulu ndiponso zowononga mu Iguputo monse,+ kwa Farao ndi kwa anthu onse amʼnyumba mwake, ife tikuona.+
3 Koma ine ndidzalola Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zodabwitsa zochuluka mʼdziko la Iguputo.+
33 Ndiyeno Aiguputo anayamba kuumiriza anthuwo kuti achoke mʼdzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+
22 Choncho Yehova anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zazikulu ndiponso zowononga mu Iguputo monse,+ kwa Farao ndi kwa anthu onse amʼnyumba mwake, ife tikuona.+