Ekisodo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno udzaike guwa lansembe zofukiza lagolide+ patsogolo pa likasa la Umboni, nʼkuika nsalu yotchinga pakhomo la chihema.+
5 Ndiyeno udzaike guwa lansembe zofukiza lagolide+ patsogolo pa likasa la Umboni, nʼkuika nsalu yotchinga pakhomo la chihema.+