2 “Uwerenge+ gulu lonse la Aisiraeli* mogwirizana ndi mabanja awo, potengera nyumba za makolo awo, nʼkulemba mayina awo. Uwerenge amuna onse, mmodzi ndi mmodzi.
15 Kenako Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira mʼmawa mpaka nthawi yomwe anakonza, moti anthu 70,000 anafa,+ kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+