Ekisodo 40:30, 31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anaika beseni pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe nʼkuthiramo madzi osamba.+ 31 Mose, Aroni ndi ana ake ankasamba mʼmanja ndi mapazi awo pamenepo. Aheberi 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tiyeni tifike kwa Mulungu ndi mtima wonse komanso tili ndi chikhulupiriro chonse, chifukwa mitima yathu yayeretsedwa* kuti tisakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa mʼmadzi oyera.+
30 Kenako anaika beseni pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe nʼkuthiramo madzi osamba.+ 31 Mose, Aroni ndi ana ake ankasamba mʼmanja ndi mapazi awo pamenepo.
22 tiyeni tifike kwa Mulungu ndi mtima wonse komanso tili ndi chikhulupiriro chonse, chifukwa mitima yathu yayeretsedwa* kuti tisakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa mʼmadzi oyera.+