Ekisodo 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zopereka zimene ukuyenera kulandira kwa iwo ndi izi: golide,+ siliva,+ kopa,*+ Ekisodo 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 mafuta a nyale,+ basamu wopangira mafuta odzozera+ ndi zofukiza zonunkhira.+