Ekisodo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika+ ndi mafuta onunkhira abwino kwambiri,+ osakanizidwa mwaluso.* Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+ Chivumbulutso 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atatenga mpukutuwo, angelo 4 ndi akulu 24 aja+ anagwada nʼkuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze komanso mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. (Zofukizazo zikuimira mapemphero a oyera.)+
29 Anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika+ ndi mafuta onunkhira abwino kwambiri,+ osakanizidwa mwaluso.*
2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
8 Atatenga mpukutuwo, angelo 4 ndi akulu 24 aja+ anagwada nʼkuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze komanso mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. (Zofukizazo zikuimira mapemphero a oyera.)+