-
Ekisodo 30:31, 32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Uuze Aisiraeli kuti, ‘Mafuta awa akhale mafuta anga ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika mʼmibadwo yanu yonse.+ 32 Musapake mafuta amenewa pakhungu la munthu aliyense, ndipo musapange mafuta ofanana nawo pogwiritsa ntchito zinthu zopangira mafutawa. Mafuta amenewa ndi opatulika. Apitirizebe kukhala opatulika kwa inu.
-