Deuteronomo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yehova anandipatsa miyala iwiri yosema imene Mulungu analembapo ndi chala chake. Pamiyala imeneyi panali mawu onse amene Yehova analankhula nanu mʼphiri, kuchokera mʼmoto, pa tsiku limene munasonkhana kumeneko.+
10 Kenako Yehova anandipatsa miyala iwiri yosema imene Mulungu analembapo ndi chala chake. Pamiyala imeneyi panali mawu onse amene Yehova analankhula nanu mʼphiri, kuchokera mʼmoto, pa tsiku limene munasonkhana kumeneko.+