Ekisodo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Yehova anafika pamwamba pa phiri la Sinai. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo ndipo Mose anakweradi.+ Ekisodo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kwera mʼphiri muno ufike kwa ine ndipo ukhalebe momʼmuno. Ndikupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+
20 Choncho Yehova anafika pamwamba pa phiri la Sinai. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo ndipo Mose anakweradi.+
12 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kwera mʼphiri muno ufike kwa ine ndipo ukhalebe momʼmuno. Ndikupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+