Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho okondedwa anga, pewani* kulambira mafano.+ 1 Yohane 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana anga okondedwa, muzipewa mafano.+