Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+ Luka 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Izi zinali zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Yehova* kuti: “Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* adzakhala woyera kwa Yehova.”*+
2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+
23 Izi zinali zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Yehova* kuti: “Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* adzakhala woyera kwa Yehova.”*+