Ekisodo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zimene muzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe ndi wa nkhosa yanu ndi izi:+ Azikhala ndi mayi ake masiku 7. Pa tsiku la 8 muzimupereka kwa ine.+
30 Zimene muzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe ndi wa nkhosa yanu ndi izi:+ Azikhala ndi mayi ake masiku 7. Pa tsiku la 8 muzimupereka kwa ine.+