Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komanso muzichita Chikondwerero cha Zokolola.* Muzikondwerera zipatso zoyamba kucha za mbewu zimene munadzala mʼminda yanu, yomwe ndi ntchito ya manja anu.+ Muzichitanso Chikondwerero cha Kututa* kumapeto kwa chaka, mukamatuta zipatso zamʼmunda, yomwe ndi ntchito ya manja anu.+

  • Levitiko 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 la mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova Chikondwerero cha Misasa kwa masiku 7.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena