Ekisodo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadzasunge nyama iliyonse kuti ifike mʼmawa. Koma iliyonse yotsala kufika mʼmawa mudzaipsereze pamoto.+ Numeri 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Asamasiye nyama iliyonse mpaka mʼmamawa,+ ndipo asamaphwanye fupa lake lililonse.+ Aziikonza motsatira malamulo onse a Pasika.
10 Musadzasunge nyama iliyonse kuti ifike mʼmawa. Koma iliyonse yotsala kufika mʼmawa mudzaipsereze pamoto.+
12 Asamasiye nyama iliyonse mpaka mʼmamawa,+ ndipo asamaphwanye fupa lake lililonse.+ Aziikonza motsatira malamulo onse a Pasika.