2 Akorinto 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Malamulo amene amachititsa kuti munthu afe, amenenso analembedwa pamiyala,+ anabwera ndi ulemerero waukulu kwambiri moti Aisiraeli sanathe kuyangʼanitsitsa nkhope ya Mose chifukwa inkawala ndi ulemerero+ umene unatha patapita nthawi.
7 Malamulo amene amachititsa kuti munthu afe, amenenso analembedwa pamiyala,+ anabwera ndi ulemerero waukulu kwambiri moti Aisiraeli sanathe kuyangʼanitsitsa nkhope ya Mose chifukwa inkawala ndi ulemerero+ umene unatha patapita nthawi.