Ekisodo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa tsiku lotsatira, Mose anauza anthuwo kuti: “Mwachita tchimo lalikulu kwambiri. Choncho ndipita kuphiri kwa Yehova kuti mwina ndingakamuchonderere kuti akukhululukireni tchimo lanu.”+
30 Pa tsiku lotsatira, Mose anauza anthuwo kuti: “Mwachita tchimo lalikulu kwambiri. Choncho ndipita kuphiri kwa Yehova kuti mwina ndingakamuchonderere kuti akukhululukireni tchimo lanu.”+