Levitiko 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo azibweretsa kwa wansembe nkhosa yamphongo yopanda chilema kuti ikhale nsembe yake yakupalamula, yoperekedwa kwa Yehova, mogwirizana ndi mtengo umene wagamulidwa kuti ikhale nsembe yakupalamula.+
6 Ndipo azibweretsa kwa wansembe nkhosa yamphongo yopanda chilema kuti ikhale nsembe yake yakupalamula, yoperekedwa kwa Yehova, mogwirizana ndi mtengo umene wagamulidwa kuti ikhale nsembe yakupalamula.+