Levitiko 22:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukafuna kupereka nsembe yoyamikira kwa Yehova+ muziipereka mʼnjira yakuti Mulungu asangalale nanu. 30 Muziidya tsiku lomwelo. Musasiye nyama iliyonse mpaka mʼmamawa.+ Ine ndine Yehova.
29 Mukafuna kupereka nsembe yoyamikira kwa Yehova+ muziipereka mʼnjira yakuti Mulungu asangalale nanu. 30 Muziidya tsiku lomwelo. Musasiye nyama iliyonse mpaka mʼmamawa.+ Ine ndine Yehova.