Levitiko 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Akatero aziika dzanja lake pamutu pa mbuzi yaingʼonoyo ndipo aziipha pamaso pa Yehova,+ pamalo ophera nyama ya nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yamachimo. Levitiko 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mafuta onse a mbuziyo aziwawotcha paguwa lansembe mofanana ndi mafuta a nsembe yamgwirizano.+ Pamenepo wansembe aziphimba tchimo la mtsogoleriyo, ndipo adzakhululukidwa.
24 Akatero aziika dzanja lake pamutu pa mbuzi yaingʼonoyo ndipo aziipha pamaso pa Yehova,+ pamalo ophera nyama ya nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yamachimo.
26 Mafuta onse a mbuziyo aziwawotcha paguwa lansembe mofanana ndi mafuta a nsembe yamgwirizano.+ Pamenepo wansembe aziphimba tchimo la mtsogoleriyo, ndipo adzakhululukidwa.