Genesis 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma musadye+ nyama limodzi ndi magazi ake,+ chifukwa magaziwo ndi moyo wake. Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu aliyense wamʼnyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzadana naye ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake. Levitiko 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngati munthu wa Chiisiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu wapita kokasaka, ndipo wagwira nyama kapena mbalame imene munaloledwa kuti muzidya, azithira magazi ake pansi+ nʼkuwakwirira ndi dothi. Deuteronomo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma mungokhala otsimikiza mtima kuti musadye magazi,+ chifukwa magazi ndi moyo,+ ndipo musamadye nyama limodzi ndi moyo wake. Machitidwe 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ chiwerewere,*+ zopotola* ndi magazi.+ Machitidwe 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola*+ ndi chiwerewere.*+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri, zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”*
10 Munthu aliyense wamʼnyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzadana naye ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.
13 Ngati munthu wa Chiisiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu wapita kokasaka, ndipo wagwira nyama kapena mbalame imene munaloledwa kuti muzidya, azithira magazi ake pansi+ nʼkuwakwirira ndi dothi.
23 Koma mungokhala otsimikiza mtima kuti musadye magazi,+ chifukwa magazi ndi moyo,+ ndipo musamadye nyama limodzi ndi moyo wake.
20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ chiwerewere,*+ zopotola* ndi magazi.+
29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola*+ ndi chiwerewere.*+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri, zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”*