Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+ Aefeso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.”+ Limeneli ndi lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo. Lonjezo lake ndi lakuti: Aheberi 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Bambo athu otibereka ankatilanga ndipo tinkawalemekeza. Ndiye kuli bwanji Atate wa moyo wathu wauzimu? Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+
12 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+
2 “Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.”+ Limeneli ndi lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo. Lonjezo lake ndi lakuti:
9 Bambo athu otibereka ankatilanga ndipo tinkawalemekeza. Ndiye kuli bwanji Atate wa moyo wathu wauzimu? Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+