Ekisodo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muzikumbukira tsiku la Sabata ndipo muziliona kuti ndi lopatulika.+ Ekisodo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa kwa masiku 6 Yehova anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndipo anayamba kupuma pa tsiku la 7.+ Nʼchifukwa chake Yehova anadalitsa tsiku la Sabata ndipo analipanga kukhala lopatulika. Ekisodo 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Uuze Aisiraeli kuti, ‘Muonetsetse kuti mukusunga masiku anga a sabata.+ Chimenechi ndi chizindikiro pakati pa ine ndi inu mʼmibadwo yanu yonse, kuti mudziwe kuti ine Yehova ndakusankhani kukhala opatulika. Luka 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anapitiriza kuwauza kuti: “Mwana wa munthu ndi Mbuye wa Sabata.”+
11 Chifukwa kwa masiku 6 Yehova anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndipo anayamba kupuma pa tsiku la 7.+ Nʼchifukwa chake Yehova anadalitsa tsiku la Sabata ndipo analipanga kukhala lopatulika.
13 “Uuze Aisiraeli kuti, ‘Muonetsetse kuti mukusunga masiku anga a sabata.+ Chimenechi ndi chizindikiro pakati pa ine ndi inu mʼmibadwo yanu yonse, kuti mudziwe kuti ine Yehova ndakusankhani kukhala opatulika.