Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muzimupatsa malipiro ake tsiku lomwelo dzuwa lisanalowe,+ chifukwa iye ndi wosauka ndipo akudalira malipiro ake omwewo kuti akhale ndi moyo. Mukapanda kutero adzafuula kwa Yehova chifukwa cha zimene inuyo mwamuchitira ndipo mudzapezeka kuti mwachimwa.+

  • Yeremiya 22:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsoka kwa munthu amene amamanga nyumba yake

      Komanso zipinda zake zamʼmwamba mopanda chilungamo.

      Amene amagwiritsa anthu ntchito kwaulere,

      Ndipo amakana kuwapatsa malipiro awo.+

  • Yakobo 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena