Deuteronomo 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Wotembereredwa ndi munthu wosocheretsa munthu amene ali ndi vuto losaona.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
18 ‘Wotembereredwa ndi munthu wosocheretsa munthu amene ali ndi vuto losaona.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)