Deuteronomo 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼmunda wanu wa mpesa musamadzalemo mbewu zamitundu ina,+ chifukwa mukachita zimenezo zokolola zanu zonse komanso mphesa zanu zidzaperekedwa kumalo opatulika.
9 Mʼmunda wanu wa mpesa musamadzalemo mbewu zamitundu ina,+ chifukwa mukachita zimenezo zokolola zanu zonse komanso mphesa zanu zidzaperekedwa kumalo opatulika.