1 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Sauli anafa chifukwa chakuti anasonyeza kuti ndi wosakhulupirika pamaso pa Yehova. Iye sanamvere mawu a Yehova+ komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu+
13 Choncho Sauli anafa chifukwa chakuti anasonyeza kuti ndi wosakhulupirika pamaso pa Yehova. Iye sanamvere mawu a Yehova+ komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu+