Ekisodo 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Aliyense wotemberera bambo ake kapena mayi ake aziphedwa.+ Deuteronomo 27:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Wotembereredwa ndi munthu wonyoza bambo ake kapena mayi ake.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Miyambo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aliyense amene amatemberera bambo ake komanso mayi ake,Nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+ Mateyu 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wolankhula mawu achipongwe kwa bambo ake kapena mayi ake aziphedwa.’+
16 ‘Wotembereredwa ndi munthu wonyoza bambo ake kapena mayi ake.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wolankhula mawu achipongwe kwa bambo ake kapena mayi ake aziphedwa.’+