Levitiko 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usagone ndi mkazi wa bambo ako,+ chifukwa kuchita zimenezo nʼkuchititsa manyazi bambo ako.* Deuteronomo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wachititsa manyazi bambo akewo.’*+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
20 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wachititsa manyazi bambo akewo.’*+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)