Levitiko 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usagone ndi mchemwali wako, kaya ndi mwana wamkazi wa bambo ako kapena mwana wamkazi wa mayi ako. Kaya munabadwira mʼbanja limodzi kapena anabadwira mʼbanja lina.+ Deuteronomo 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mchemwali wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
9 Usagone ndi mchemwali wako, kaya ndi mwana wamkazi wa bambo ako kapena mwana wamkazi wa mayi ako. Kaya munabadwira mʼbanja limodzi kapena anabadwira mʼbanja lina.+
22 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mchemwali wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)