Levitiko 18:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usagone ndi mchemwali wa bambo ako. Ameneyo ndi wachibale wa bambo ako.+ 13 Usagone ndi mchemwali wa mayi ako, chifukwa ndi wachibale wa mayi ako.
12 Usagone ndi mchemwali wa bambo ako. Ameneyo ndi wachibale wa bambo ako.+ 13 Usagone ndi mchemwali wa mayi ako, chifukwa ndi wachibale wa mayi ako.