-
Deuteronomo 5:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli onse nʼkuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.
-