Levitiko 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ili likhale lamulo lokhudza wakhate pa tsiku limene adzamubweretse kwa wansembe+ pa nthawi yoti ayeretsedwe. Levitiko 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno munthuyo akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera. Kenako azichapa zovala zake nʼkusamba madzi otunga kumtsinje, ndipo iye adzakhala woyera.+
2 “Ili likhale lamulo lokhudza wakhate pa tsiku limene adzamubweretse kwa wansembe+ pa nthawi yoti ayeretsedwe.
13 Ndiyeno munthuyo akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera. Kenako azichapa zovala zake nʼkusamba madzi otunga kumtsinje, ndipo iye adzakhala woyera.+