Levitiko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zamoyo zimenezi nʼzimene mungadzidetse nazo. Aliyense wokhudza zamoyo zimenezi zitafa adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Levitiko 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Musamadziipitse ndi zamoyo zilizonse zimene zimapezeka zambirizi ndipo musamadzidetse nazo nʼkukhala odetsedwa.+
24 Zamoyo zimenezi nʼzimene mungadzidetse nazo. Aliyense wokhudza zamoyo zimenezi zitafa adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+
43 Musamadziipitse ndi zamoyo zilizonse zimene zimapezeka zambirizi ndipo musamadzidetse nazo nʼkukhala odetsedwa.+