Ekisodo 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti awaike* kukhala ansembe nʼkuwayeretsa. Koma munthu wamba* asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+
33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti awaike* kukhala ansembe nʼkuwayeretsa. Koma munthu wamba* asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+