Numeri 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aisiraeli ali mʼchipululumo, tsiku lina anapeza munthu wina akutola nkhuni pa tsiku la Sabata.+ Numeri 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi.+ Gulu lonse likamuponye miyala kunja kwa msasa.”+ Deuteronomo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kumuponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+
35 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi.+ Gulu lonse likamuponye miyala kunja kwa msasa.”+
7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kumuponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+