Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma mʼchaka cha 7 dzikolo lizidzasunga sabata lopuma pa zonse, sabata la Yehova. Musamadzadzale mbewu mʼminda yanu kapena kudulira mitengo yanu ya mpesa. 5 Musamadzakolole mbewu zomera zokha kuchokera pa mbewu zimene munakolola chaka chapita, ndipo musamadzakololenso mphesa za mʼmitengo yanu yosadulirayo. Chaka chimenecho dziko lizidzapuma pa zonse.

  • Mateyu 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti: Siyani kudera nkhawa za moyo wanu,+ kuti mudzadya chiyani kapena kuti mudzamwa chiyani kapenanso kudera nkhawa za matupi anu kuti mudzavala chiyani.+ Kodi moyo si wofunika kwambiri kuposa chakudya ndipo kodi thupi si lofunika kwambiri kuposa chovala?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena