1 Mafumu 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Naboti anayankha Ahabu kuti: “Ndikaiona nkhaniyi mmene Yehova akuionera, nʼkosayenera kuti ndikupatseni cholowa cha makolo anga.”+
3 Koma Naboti anayankha Ahabu kuti: “Ndikaiona nkhaniyi mmene Yehova akuionera, nʼkosayenera kuti ndikupatseni cholowa cha makolo anga.”+