Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake.
24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake.