Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezera kuti: “Ndaona mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuvutikira, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Ndikudziwa bwino ululu umene akumva.+ Aefeso 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi. Musamawaopseze chifukwa mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo, ali kumwamba+ ndipo alibe tsankho. Akolose 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu anthu amene ndinu ambuye, muzichitira akapolo anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, chifukwa mukudziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+
7 Yehova anawonjezera kuti: “Ndaona mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuvutikira, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Ndikudziwa bwino ululu umene akumva.+
9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi. Musamawaopseze chifukwa mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo, ali kumwamba+ ndipo alibe tsankho.
4 Inu anthu amene ndinu ambuye, muzichitira akapolo anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, chifukwa mukudziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+