Danieli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngakhale atapanda kutipulumutsa, dziwani mfumu kuti ife sititumikira milungu yanu kapena kulambira fano lagolide limene mwaimika.”+ 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho okondedwa anga, pewani* kulambira mafano.+
18 Koma ngakhale atapanda kutipulumutsa, dziwani mfumu kuti ife sititumikira milungu yanu kapena kulambira fano lagolide limene mwaimika.”+