Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ndidzakutengani kuti mukhale anthu anga, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndikukupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani. 2 Akorinto 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo pali kugwirizana kotani pakati pa kachisi wa Mulungu ndi mafano?+ Chifukwa ifeyo ndife kachisi wa Mulungu wamoyo,+ ngati mmene Mulungu ananenera kuti: “Ndidzakhala pakati pawo+ ndiponso ndidzayenda pakati pawo. Ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.”+
7 Choncho ndidzakutengani kuti mukhale anthu anga, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndikukupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani.
16 Ndipo pali kugwirizana kotani pakati pa kachisi wa Mulungu ndi mafano?+ Chifukwa ifeyo ndife kachisi wa Mulungu wamoyo,+ ngati mmene Mulungu ananenera kuti: “Ndidzakhala pakati pawo+ ndiponso ndidzayenda pakati pawo. Ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.”+