Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza ankawapereka mʼmanja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu amene ankadana nawo aziwalamulira.+ Maliro 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano adani ake akumulamulira. Iwo sakuda nkhawa.+ Yehova wamuchititsa kuti akhale ndi chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa machimo ake.+ Ana ake agwidwa ndi adani ndipo atengedwa kupita ku ukapolo.+
41 Mobwerezabwereza ankawapereka mʼmanja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu amene ankadana nawo aziwalamulira.+
5 Tsopano adani ake akumulamulira. Iwo sakuda nkhawa.+ Yehova wamuchititsa kuti akhale ndi chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa machimo ake.+ Ana ake agwidwa ndi adani ndipo atengedwa kupita ku ukapolo.+