Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Afesa tirigu koma akolola minga.+

      Agwira ntchito yotopetsa koma osapeza phindu lililonse.

      Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawo

      Chifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.”

  • Hagai 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mwadzala mbewu zambiri, koma mukukolola zochepa.+ Mukudya, koma simukukhuta. Mukumwa koma simukukhutira. Mukuvala zovala, koma simukumva kutenthera. Ndipo amene akugwira ganyu akuika ndalama zake mʼmatumba obowoka.’”

  • Hagai 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ‘Nʼchifukwa chake kumwamba sikunakugwetsereni mame ndipo dziko lapansi silinakupatseni zokolola.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena