Deuteronomo 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzalefuka ndi njala+Ndipo adzavutika ndi kutentha thupi koopsa komanso adzawonongedwa nʼkutheratu.+ Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali+Komanso njoka zapoizoni za mʼfumbi. Yeremiya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ndidzawabweretsera masoka okwanira 4,’*+ akutero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, mbalame zamumlengalenga komanso zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.+
24 Adzalefuka ndi njala+Ndipo adzavutika ndi kutentha thupi koopsa komanso adzawonongedwa nʼkutheratu.+ Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali+Komanso njoka zapoizoni za mʼfumbi.
3 “‘Ndidzawabweretsera masoka okwanira 4,’*+ akutero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, mbalame zamumlengalenga komanso zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.+