-
Yesaya 9:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Munthu adzacheka zimene zili kumbali yakumanja
Koma adzakhalabe ndi njala.
Ndipo munthu adzadya zimene zili kumanzere kwake
Koma sadzakhuta.
Aliyense adzadya mnofu wa dzanja lake,
-
Mika 6:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Mudzanyamula zinthu kuti mukazisunge pabwino, koma simudzatha kuziteteza.
Zimene mudzatenge, ndidzazipereka kwa adani anu kuti aziwononge.
-
-
-